Exodus 4:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake Chauta adakumana naye Mose pa njira pa malo a chigono, nafuna kumupha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kunali panjira, kuchigono, Yehova anakomana naye, nafuna kumupha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pambuyo pake Mose ali mʼnjira, pamalo wogona, Yehova anakumana naye, ndipo anafuna kumupha.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kunali panjira, kucigono, Yehova anakomana naye, nafuna kumupha.