Exodus 4:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo Chauta adati, “Akakapanda kukukhulupirira, osasamala chizindikiro choyambacho, akakhulupirira ndithu chifukwa cha chizindikiro chachiŵiricho.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kudzatero, ngati sakhulupirira iwe, ndi kusamvera mau a chizindikiro choyamba, adzakhulupirira mau a chizindikiro chotsirizachi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono Yehova anati “Akakapanda kukukhulupirira, osalabadira chozizwitsa choyambacho, akakhulupirira ndithu chifukwa cha chozizwitsa chachiwiricho.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kudzatero, ngati sakhulupirira iwe, ndi kusamvera mau a cizindikilo coyamba, adzakhulupirira mau a cizindikilo cotsirizaci.