Exodus 40:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero pa tsiku loyamba la mwezi woyamba chaka chachiŵiri, malo opatulika adautsidwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kunali, mwezi woyamba wa chaka chachiwiri, tsiku loyamba la mwezi, anautsa Kachisi,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kotero anayimika chihema tsiku loyamba la mwezi woyamba mʼchaka chachiwiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kunali, mwezi woyamba wa caka caciwiri, tsiku loyamba la mwezi, anautsa kacisi.