Exodus 40:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono m'chihema chamsonkhanomo adaikamo tebulo, chakumpoto kwa malo opatulika, kunja kwa nsalu yochinga ija,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anaika gomelo m'chihema chokomanako, pa mbali ya kumpoto ya Kachisi, kunja kwa nsalu yotchinga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mose anayika tebulo mu tenti ya msonkhano kumpoto kwa chihema, kunja kwa katani,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anaika gomelo m'cihema cokomanako, pa mbali ya kumpoto ya kacisi, kunja kwa nsaru yocinga.