Exodus 5:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero anthu aja adamwazikira m'dziko lonse la Ejipito kukafunafuna udzuwo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo anthuwo anabalalika m'dziko lonse la Ejipito kufuna chiputu ngati udzu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kotero anthuwo anamwazikana mʼdziko lonse la Igupto kukamweta udzu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo anthuwo anabalalika m'dziko lonse la Aigupto kufuna ciputu ngati udzu.