Exodus 5:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Farao adaŵayankha anthuwo kuti, “Ndinu alesi inu, alesi zedi, nchifukwa chake mukuti, ‘Tiyeni tipite tikapereke nsembe kwa Chauta.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma iye anati, Aulesi inu, aulesi: chifukwa chake mulikunena, Timuke, timphere nsembe Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Farao anati, “Ulesi, inu ndinu alesi! Nʼchifukwa chake mukumanena kuti, ‘Mutilole tipite kukapereka nsembe kwa Yehova.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma iye anati, Aulesi inu, aulesi: cifukwa cace mulikunena, Timuke, timphere nsembe Yehova.