Exodus 5:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chokani apa, bwererani ku ntchito yanu. Udzu asakupatseni, koma chiŵerengero cha njerwa ndi chonchija ndithu basi.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mukani tsopano, gwirani ntchito; pakuti sadzakupatsani udzu, koma muonetse chiwerengero chake cha njerwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pitani tsopano kuntchito. Simudzapatsidwanso udzu komabe muyenera kuwumba muyeso wanu wovomerezeka wa njerwa.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mukani tsopano, gwirani nchito; pakuti sadzakupatsani udzu, koma muonetse ciwerengero cace ca njerwa.