Exodus 5:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho Mose adapemphera kwa Chauta nati, “Inu Chauta, chifukwa chiyani mukuzunza anthu anu? Nanga ine mudanditumiranji?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo Mose anabwerera namka kwa Yehova, nati, Ambuye, mwawachitiranji choipa anthuwa? Mwandituma bwanji?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mose anabwerera kwa Yehova ndipo anati, “Chonde Ambuye, chifukwa chiyani mukuzunza anthu anu? Kodi munanditumira zimenezi?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo Mose anabwerera namka kwa Yehova, nati, Ambuye, mwawacitiranji coipa anthuwa? mwandituma bwanji?