Exodus 5:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Muŵagwiritse ntchito yakalavulagaga anthu ameneŵa, kuti azitanganidwa ndi ntchito m'malo momangomvera zabodza.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ilimbike ntchito pa amunawo, kuti aigwiritsitse, asasamalire mau amabodza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Muwakhawulitse ndi ntchito anthu amenewa kuti azitanganidwa, asakhale ndi mpata omvera zabodza.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ilimbike nchito pa amunawo, kuti aigwiritsitse, asasamalire mau amabodza.