Exodus 6:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana a Simeoni naŵa: Yemuwele, Yamini, Ohadi, Yakini, Zohari ndi Shaulo mwana wa kwa mkazi wa ku Kanani. Ameneŵa ndiwo a m'banja la Simeoni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi ana amuna a Simeoni ndiwo: Yemuwele, ndi Yamini, ndi Ohadi, Yakini, ndi Zohari, ndi Shaulo mwana wa mkazi wa Mkanani; amene ndiwo mabanja a Simeoni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana a Simeoni anali Yemueli, Yamini, Ohadi, Yakini, Zohari ndi Saulo mwana wa kwa mkazi wa Chikanaani. Awa anali mafuko a Simeoni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi ana amuna a Simeoni ndiwo: Yemweli, ndi Yamini, ndi Ohadi, Yakini, ndi Zohari, ndi Sauli mwana wa mkazi wa m'Kanani; amene ndiwo mabanja a Simeoni.