Exodus 6:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana a Geresoni naŵa: Libini ndi Simeyi pamodzi ndi mabanja ao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ana amuna a Geresoni ndiwo: Libini ndi Simei, mwa mabanja ao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana a Geresoni, mwa mafuko awo, anali Libini ndi Simei.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ana amuna a Gerisoni ndiwo: Libni ndi Simei, mwa mabanja ao.