Exodus 6:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana a Merari naŵa: Mali ndi Musi. Ameneŵa ndiwo mabanja a Levi pamodzi ndi zidzukulu zao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ana amuna a Merari ndiwo: Mali ndi Musi. Amenewo ndiwo mabanja a Levi mwa kubadwa kwao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana a Merari anali Mali ndi Musi. Awa anali mafuko a Levi monga mwa mibado yawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ana amuna a Merai ndiwo: Mali ndi Musi. Amenewo ndiwo mabanja a Levi mwa kubadwa kwao.