Exodus 6:26 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mose ndi Aroni ndi omwe aja amene Chauta adaŵauza kuti, “Atulutseni Aisraele m'dziko la Ejipito mwa magulumagulu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Omwewo ndiwo Aroni ndi Mose amene Yehova ananena nao, Tulutsani ana a Israele m'dziko la Ejipito mwa makamu ao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Aaroni ndi Mose ndi aja amene Yehova anawawuza kuti, “Tulutsani Aisraeli mu Igupto mʼmagulu awo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Omwewo ndiwo Aroni ndi Mose amene Yehova ananena nao, Turutsani ana a Israyeli m'dziko la Aigupto mwa makamu ao.