Exodus 6:28 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene Chauta adalankhula ndi Mose ku dziko la Ejipito,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kunali, tsiku limene Yehova ananena ndi Mose m'dziko la Ejipito,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsopano pamene Yehova anayankhula kwa Mose mu Igupto,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kunali, tsiku limene Yehova ananena ndi Mose m'dziko la Aigupto,