Exodus 6:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidachita nawo chipangano ndi kuŵalonjeza kuti ndidzaŵapatsa dziko la Kanani, momwe adakhalamo kale ngati alendo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndinakhazikitsanso nao chipangano changa, kuwapatsa dziko la Kanani, dziko la maulendo ao, anali alendo m'mwemo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndinakhazikitsa pangano langa ndi iwo kuwalonjeza kuti ndidzawapatsa dziko la Kanaani kumene anakhalako kale ngati alendo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndinakhazikitsanso nao cipangano canga, kuwapatsa dziko la Kanani, dziko la maulendo ao, anali alendo m'mwemo.