Exodus 7:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo Aejipito adzadziŵa kuti Ine ndine Chauta, ndikadzaŵakantha ndi dzanja langa ndi kutulutsa Aisraele m'dziko mwaomo.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Aejipito adzadziwa kuti Ine ndine Yehova, pakutambasula Ine dzanja langa pa Aejipito, ndikutulutsa ana a Israele pakati pao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Aigupto adzadziwa kuti Ine ndine Yehova, ndikadzatambasula dzanja langa kukantha Igupto ndi kutulutsa Aisraeli mʼdzikomo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Aaigupto adzadziwa kuti Ine ndine Yehova, pakutambasula Ine dzanja langa pa Aigupto, ndi kuturutsa ana a Israyeli pakati pao.