Exodus 8:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ukakana kuŵalola, dziko lako lonse ndidzalilanga polidzaza ndi achule.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ukakana kuwalola amuke, taona, Ine ndidzapanda dziko lako lonse ndi achule;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo ngati simulola kuti apite Ine ndidzalanga dziko lonse la Igupto polidzaza ndi achule.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ukakana kuwalola amuke, taona, Ine ndidzapanda dziko lako lonse ndi acule;