Exodus 8:27 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tiyenera kuyenda ulendo wa masiku atatu m'chipululu, kuti tikapereke nsembe kwa Chauta, Mulungu wathu, monga adatilamulira.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Timuke ulendo wa masiku atatu m'chipululu, tikamphere Yehova Mulungu wathu nsembe, monga adzanena nafe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ife tiyenera kuyenda ulendo wa masiku atatu kupita ku chipululu kukapereka nsembe kwa Yehova Mulungu wathu monga anatilamulira.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Timuke ulendo wa masiku atatu m'cipululu, tikamphere Yehova Mulungu wathu nsembe, monga adzanena nafe.