Exodus 8:32 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ngakhale pa nthaŵi imeneyinso, Farao adakhala wokanikabe, ndipo sadalole kuti Aisraele apite.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Farao anaumitsa mtima wake nthawi yomweyonso, ndipo sanalola anthu amuke.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma nthawi imeneyinso Farao anawumitsa mtima wake ndipo sanalole kuti anthu atuluke.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Farao anaumitsa mtima wace nthawi yomweyonso, ndipo sanalola anthu amuke.