Exodus 8:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma amatsenga aja nawonso adapanga ao achule ndipo adayamba kukwera pa mtunda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo alembi anachita momwemo ndi matsenga ao, nakweretsa achule pa dziko la Ejipito.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma amatsenga anachita zinthu zomwezo mʼmatsenga awo. Iwonso anatulutsa achule mʼdziko lonse la Igupto.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo alembi anacita momwemo ndi matsenga ao, nakweretsa acule pa dziko la Aigupto.