Exodus 9:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndikadasamula dzanja langa kuti ndikumenye iwe pamodzi ndi anthu ako, bwenzi tsopano nonsenu mutatha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti ndatambasula dzanja langa tsopano, kuti ndikupande iwe ndi anthu ako ndi mliri, ndi kuti uonongeke pa dziko lapansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti ndikanakhala nditatukula kale dzanja langa ndikupheratu iwe pamodzi ndi anthu ako onse pa dziko lapansi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti ndatambasula dzanja langa tsopano, kuti ndikupande iwe ndi anthu ako ndi mliri, ndi kuti uonoogeke pa dziko lapansi.