Exodus 9:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pemphera kwa Chauta kuti aŵaletse mabingu ndi matalalaŵa ndipo ndidzakulolani kuti mupite. Simudzakhalanso kuno ai.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pembani kwa Yehova; chifukwa akwanira ndithu mabingu a Mulungu ndi matalala; ndipo ndidzakulolani mumuke, osakhalanso.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Upemphere kwa Mulungu chifukwa mabingu ndi matalala atikwana. Ine ndidzakulolani kuti mupite. Simuyenera kukhalabe kuno.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pembani kwa Yehova; cifukwa akwanira ndithu mabingu a Mulungu ndi matalala; ndipo ndidzakulolani mumuke, osakhalanso.