Exodus 9:30 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komabe ndikudziŵa kuti inu ndi nduna zanu simukuwopa Chauta.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma inu ndi anyamata anu ndidziwa kuti simudzayamba kuopa nkhope ya Yehova Mulungu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma ine ndikudziwa kuti inu ndi nduna zanu simukuopabe Yehova Mulungu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma inu ndi anyamata anu ndidziwa kuti simudzayamba kuopa nkhope ya Yehova Mulungu.