Exodus 9:32 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma tirigu ndi rayi sizidaonongeke, chifukwa zimenezi amabzala mochedwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma tirigu ndi rai sizinayoyoka popeza amabzala m'mbuyo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma tirigu ndi mchewere sizinawonongeke chifukwa zimakhwima mochedwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma tirigu ndi rai sizinayoyoka popeza amabzala m'mbuyo.