Exodus 9:35 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adakhala wokanika kwambiri, ndipo sadalole kuti Aisraele apite monga momwe Chauta adaauzira Mose muja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Potero mtima wa Farao unalimba, ndipo sanalole ana a Israele amuke; monga Yehova adalankhula mwa Mose.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho Farao sanalole kuti Aisraeli apite monga momwe Yehova anamuwuzira Mose.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Potero mtima wa Farao unalimba, ndipo sanalola ana a Israyeli amuke; monga Yehova adalankhula mwa Mose.