Exodus 9:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta waika nthaŵi, ndipo akunena kuti zimenezi azichita maŵa.’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yehova anaika nthawi yakuti, nati, Mawa Yehova adzachita chinthu ichi m'dzikomu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova anayika nthawi ndipo anati, “Yehova adzachita zimenezi mmawa mʼdziko muno.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yehova anaika nthawi yakuti, nati, Mawa Yehova adzacita cinthu ice m'dzikomu.