Ezekiel 1:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kulikonse kumene mzimu wake unkaziyendetsa, zilengolengozo zinkapita kumeneko. Mikombero ija nayonso inkapita nazo pamodzi, chifukwa chakuti mzimu wa zilengolengozo ndiwo unkayendetsa mikomberoyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kuli konse mzimu ukuti umuke, zinamuka komwe mzimu ukuti umuke; ndi njingazi zinanyamuka pambali pa izi; pakuti mzimu wa zamoyozo unali m'njingazo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kulikonse kumene mzimu wake unkazitsogolera, zamoyozo zinkapita komweko. Ndipo mikombero ija inkapita nawo pamodzi popeza kuti mzimu wa zamoyozo ndiwo umayendetsa mikombero ija.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuli konse mzimu ukuti umuke, zinamuka komwe mzimu ukuti umuke; ndi njingazi zinanyamuka pambali pa izo; pakuti mzimu wa zamoyozo unali m'njingazo.