Ezekiel 1:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamwamba pa mitu ya zilengolengozo panali chinthu chonga thambo loŵala looneka ngati galasi lochezimira, loyalidwa pamwamba pa mitu yake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi pa mitu ya zamoyozi panali chifaniziro cha thambo, monga mawalidwe a krustalo woopsa, loyalika pamwamba pamitu pao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamwamba pa mitu ya zamoyozo panali chinthu chonga thambo, lowala ndipo kunyezimira kwake ngati galasi loyangʼanitsa ku dzuwa, loyalidwa pamwamba pa mitu yake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi pa mitu ya zamoyozi panali cifaniziro ca thambo, monga mawalidwe a krustalo woopsa, loyalika pamwamba pamitu pao.