Ezekiel 1:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zilengolengozo zidaatambalitsa mapiko ake m'munsi mwa thambo lija, mapiko ake ena kumakhudzana, mapiko aŵiri kumaphimbira thupili.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi pansi pa thambolo mapiko ao analunjikana, lina kulunjika kulinzake; chilichonse chinali nao mapiko awiri akuphimba matupi ao, chakuno ndi chauko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zamoyozo zinatambalitsa mapiko ake mʼmunsi mwa thambo lija, mapiko ake ena kumakhudzana, mapiko awiri kumaphimba thupi lake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi pansi pa thambolo mapiko ao analunjikana, lina kulunjika ku linzace; ciri conse cinali nao mapiko awiri akuphimba matupi ao, cakuno ndi cauko.