Ezekiel 1:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nthaŵi imeneyo Chauta adandipatsira uthenga ine Ezekiele, wansembe, mwana wa Buzi, m'mphepete mwa mtsinje wa Kebara, m'dziko la Ababiloni. Ndipo ndidamva mphamvu zake zikundifikira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
anadzadi mau a Yehova kwa Ezekiele wansembe, mwana wa Buzi, m'dziko la Ababiloni kumtsinje Kebara; ndi pomwepo dzanja la Yehova lidamkhalira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova anayankhula ndi wansembe Ezekieli, mwana wa Buzi, mʼmbali mwa mtsinje wa Kebara mʼdziko la Ababuloni. Dzanja la Yehova linali pa iye kumeneko.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
anadzadi mau a Yehova kwa Ezekieli wansembe, mwana wa Buzi, m'dziko la Akasidi kumtsinje Kebara; ndi pomwepo dzanja la Yehova lidamkhalira.