Ezekiel 10:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidamva phokoso la mikombero monga lomwe ndidaalimva poyamba paja pamene ndinkaona zinthu m'masomphenya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kunena za njingazi, wina anazifuulira, ndili chimvere ine, Kunkhulirani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndinamva mikombero ikutchedwa kuti, “mikombero yakamvuluvulu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kunena za njingazi, wina anazipfuulira, ndiri cimvere ine, Kunkhulirani.