Ezekiel 10:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zimenezi ndizo zilengolengo zimene ndidaaziwona ku mtsinje wa Kebara, kunsi kwa mpando waufumu wa Mulungu wa Israele. Ndidazindikira kuti zilengolengozo zinali akerubi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Awa ndi zamoyozo ndinaziona pansi pa Mulungu wa Israele kumtsinje Kebara, ndipo ndinadziwa kuti ndiwo akerubi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Izi ndizo zamoyo ndinaziona pansi pa Mulungu wa Israeli ku mtsinje wa Kebara, ndipo ndinazindikira kuti anali akerubi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Awa ndi zamoyozo ndinaziona pansi pa Mulungu wa Israyeli kumtsinje Kebara, ndipo ndinadziwa kuti ndiwo akerubi.