Ezekiel 10:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akerubiwo aliyense anali ndi mapiko anai ndi nkhope zinai. Analinso ndi chinthu chooneka ngati dzanja lamunthu kunsi kwa mapiko ao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yense anali nazo nkhope zinai, ndi yense mapiko anai, ndi chifaniziro cha manja a munthu pansi pa mapiko ao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kerubi aliyense anali ndi nkhope zinayi ndi mapiko anayi, ndipo kunsi kwa mapiko awo kunali chinthu chimene chimaoneka ngati manja a munthu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yense anali nazo nkhope zinai, ndi yense mapiko anai, ndi cifaniziro ca manja a munthu pansi pa mapiko ao.