Ezekiel 10:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndiye kuti kunsi kwa mapiko a akerubi kunali chinthu chooneka ngati dzanja lamunthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo panaoneka pa akerubi chonga dzanja la munthu pansi pa mapiko ao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndiye kuti kunsi kwa mapiko akerubi kumaoneka zinthu zooneka ngati manja a munthu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo panaoneka pa akerubi conga dzanja la munthu pansi pa mapiko ao.