Ezekiel 11:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo mudzadziŵa kuti Ine ndine Chauta. Simudatsate malangizo anga, simudamvere malamulo anga. Koma mwakhala mukutsata malamulo a mitundu ya anthu okuzungulirani.’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo mudzadziwa kuti Ine ndine Yehova, pakuti simunayenda m'malemba anga, kapena kuchita maweruzo anga, koma mwachita monga mwa maweruzo a amitundu okhala pozungulira panu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo inu mudzadziwa kuti Ine ndine Yehova. Inu simunatsatire malangizo anga kapena kusunga malamulo anga koma mwakhala mukutsata zochita za mitundu ina ya anthu imene yakuzungulirani.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo mudzadziwa kuti Ine ndine Yehova, pakuti simunayenda m'malemba anga, kapena kucita maweruzo anga, koma mwacita monga mwa maweruzo a amitundu okhala pozungulira panu.