Ezekiel 11:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono iwe mwana wa munthu, ulose moŵadzudzula, ulose ndithu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake uwanenere, neneratu, wobadwa ndi munthu iwe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho iwe mwana wa munthu, unenere mowadzudzula. Nenera ndithu.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace uwanenere, neneratu, wobadwa ndi munthu iwe.