Ezekiel 11:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzakutulutsani mumzimdamo, ndidzakuperekani kwa anthu akudza kuti akulangeni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndidzakutulutsani m'kati mwake, ndi kukuperekani m'manja a alendo, ndi kuchita maweruzo pakati panu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndidzakuthamangitsani mu mzinda ndipo ndidzakuperekani mʼdzanja la alendo kuti akulangeni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndidzakuturutsani m'kati mwace, ndi kukuperekani m'manja a alendo, ndi kucita maweruzo pakati panu.