Ezekiel 12:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ndidzayala ukonde pa iye ndi kumkola mu msampha wanga. Ndidzapita naye ku Babiloni, ku dziko la Akaldeya, komabe iye sadzalipenya, ndipo adzafera kumeneko.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndidzamphimba ndi ukonde wanga, nadzakodwa iye mu msampha wanga; ndipo ndidzafika naye ku Babiloni, ku dziko la Ababiloni; sadzaliona, chinkana adzafako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzayala ukonde wanga pa iye ndi kumukola mu msampha wanga. Ndidzabwera naye ku Babuloni, dziko la Akaldeya, koma sadzaliona dzikolo, ndipo adzafera kumeneko.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndidzamphimba ndi ukonde wanga, nadzakodwa iye mu msampha wanga; ndipo ndidzafika naye ku Babulo, ku dziko la Akasidi; sadzaliona, cinkana adzafako.