Ezekiel 12:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Katundu wako wopita naye ku ukapolo umtulutse masana, iwo akuwona. Ndipo madzulo, iwo akuwona ndithu, uchoke kumudzi kwanu, monga ngati ukupita ku ukapolo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Uzitulutsa akatundu ako usana pamaso pao, ngati a pa ulendo wa kundende; ndipo madzulo uzituluka wekha pamaso pao, monga amatuluka olowa kundende.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Utulutse katundu wako wopita naye ku ukapolo nthawi ya masana iwo akuona. Ndipo nthawi ya madzulo, iwo akuona, uchoke monga ngati ukupita ku ukapolo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Uziturutsa akatundu ako usana pamaso pao, ngati a pa ulendo wa kundende; ndipo madzulo uzituruka wekha pamaso pao, monga amaturuka olowa kundende.