Ezekiel 13:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo khomalo litagwa, nanga anthu sadzakufunsani kuti, ‘Kodi njereza imene mudapaka ija ili kuti tsopano?’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo taonani, litagwa linga, sadzanena nanu kodi, Lili kuti dothi munalimata nalo?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene khomalo lagwa, kodi anthu sadzakufunsani kuti, ‘Kodi njereza yemwe munapaka uja ali kuti?’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo taonani, litagwa linga, sadzanena nanu kodi, Liri kuti dothi munalimata nalo?