Ezekiel 13:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Tsono iwe mwana wa munthu, ugwepo pa nkhani ya akazi amene ali pakati pa anthu ako. Iwowo amalosa zopeka za mumtima mwao, tsono uŵadzudzule.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo iwe wobadwa ndi munthu, uziika nkhope yako itsutsane nao ana akazi a anthu ako, akunenera za m'mtima mwao, nunenere chowatsutsa,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Tsono iwe mwana wa munthu, yankhulapo pa nkhani za akazi amene ali pakati pa anthu ako. Iwo amanenera zopeka za mʼmutu mwawo. Tsono adzudzule.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo iwe wobadwa ndi munthu, uziika nkhope yako itsutsane nao ana akazi a anthu ako, akunenera za m'mtima mwao, nunenere cowatsutsa,