Ezekiel 13:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake zolosa zanu zabodza zimene mukuti mudaziwona ngati kutulo, simudzaziwonanso, ndipo simudzaombezanso. Ndidzapulumutsa anthu anga m'manja mwanu. Motero mudzadziŵa kuti Ine ndine Chauta.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
chifukwa chake simudzaonanso zopanda pake, kapena kupenda; koma ndidzalanditsa anthu anga m'manja mwanu; ndipo mudzadziwa kuti Ine ndine Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
choncho inu simudzaonanso masomphenya abodza kapena kuwombeza. Ine ndidzapulumutsa anthu anga mʼmanja mwanu. Ndipo pamenepo inu mudzadziwa kuti Ine ndine Yehova.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
cifukwa cace simudzaonanso zopanda pace, kapena kupenda; koma ndidzalanditsa anthu anga m'manja mwanu; ndipo mudzadziwa kuti Ine ndine Yehova.