Ezekiel 13:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Simudakwere khoma kuti mukakonze m'mene mudagumuka, kuti banja la Israele lidziteteze kolimba pa nkhondo, pa tsiku la Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Simunakwera kuima mopasuka, kapena kumanganso linga la nyumba ya Israele, kuima kunkhondo tsiku la Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Simunakwere khoma kuti mukakonze mʼmene munagumuka, kuti Aisraeli adziteteze kolimba pa nkhondo pa tsiku la Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Simunakwera kuima mopasuka, kapena kumanganso linga la nyumba ya Israyeli, kuima kunkhondo tsiku la Yehova.