Ezekiel 14:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsiku lina akuluakulu ena a Aisraele adadza kwa ine nadzakhala pansi pamaso panga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo anafika kwa ine akulu ena a Israele nakhala pansi pamaso panga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsiku lina ena mwa akuluakulu a Israeli anabwera kwa ine ndipo anakhala pansi pamaso panga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo anafika kwa ine akulu ena a Israyeli nakhala pansi pamaso panga.