Ezekiel 14:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Mwina ndikadatumiza nkhondo ku dziko limenelo ndi kulamula kuti ipite m'dzikomo ndi kuwononga anthu ndi nyama zomwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kapena ndikadza pa dziko ndi lupanga, ndi kuti, Lupanga lipite pakati pa dziko, kuti ndilidulire munthu ndi nyama;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Kapena ndikanatumiza lupanga mʼdzikolo ndi kunena kuti, ‘Lupanga lipite mʼdziko monse,’ ndi kuwononga anthu ake ndi nyama zomwe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kapena ndikadza pa dziko ndi lupanga, ndi kuti, Lupanga lipite pakati pa dziko, kuti ndilidulire munthu ndi nyama;