Ezekiel 15:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi mtengo umene uja nkupangira chiyani? Kodi anthu angathe kupangira chokolekapo zinthu zao?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi atengako mtengo kupanga nao ntchito? Atengako chichiri kodi kupachikapo chipangizo chilichonse?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mtengo umene uja nʼkupangira chiyani? Kodi anthu angathe kupangira chikhomo chokolekapo zinthu zawo?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi atengako mtengo kupanga nao nchito? atengako ciciri kodi kupacikapo cipangizo ciri conse?