Ezekiel 15:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngakhale usanapse, sikukadatheka kugwira nawo ntchito. Nanga nanji utapserera ndi moto, adzaugwiritsa ntchito bwanji?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taonani, pokhala wamphumphu sunayenera ntchito iliyonse, nanga utanyeketsa moto nupserera udzayeneranso ntchito iliyonse?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati pamene unali wosapsa sukanatheka kuwugwiritsa ntchito, nanga bwanji utapserera ndi moto, adzawugwiritsa ntchito bwanji?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taonani, pokhala wamphumphu sunayenera nchito iri yonse, nanga utanyeketsa moto nupserera udzayeneranso nchito iri yonse?