Ezekiel 15:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo dziko laolo ndidzalisandutsa chipululu, chifukwa chakuti iwowo sadakhulupirike. Ndikutero Ine Ambuye Chauta.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndidzasandutsa dziko chipululu; popeza anachita cholakwa, ati Ambuye Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndidzasandutsa dziko kukhala chipululu chifukwa anthu akhala osakhulupirika, akutero Ambuye Yehova.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndidzasandutsa dziko cipululu; popeza anacita colakwa, ati Ambuye Yehova.