Ezekiel 16:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Iwe mwana wa munthu, umuwonetse Yerusalemu makhalidwe ake onyansa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wobadwa ndi munthu iwe, Dziwitsa Yerusalemu zonyansa zake, nuziti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Iwe mwana wa munthu, udzudzule Yerusalemu za ntchito zake zonyansa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wobadwa ndi munthu iwe, Dziwitsa Yerusalemu zonyansa zace, nuziti,