Ezekiel 16:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chifukwa cha zigololo zako zonyansazo, udaiŵala masiku a ubwana wako, pamene unali wamaliseche, wausiŵa ndi womangovimvinizika m'magazi ako.’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pa zonyansa zako zonse ndi zigololo zako sunakumbukira masiku a ubwana wako, muja unakhala wamaliseche ndi wausiwa, wovimvinizika m'mwazi wako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chifukwa cha zadama zako zonyansazi unayiwala masiku a ubwana wako pamene unali wamaliseche, wausiwa ndiponso womangovivinizika mʼmagazi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pa zonyansa zako zonse ndi zigololo zako sunakumbukila masiku a ubwana wako, mujaunakhala wamarisece ndi wausiwa, wobvimvinizika m'mwazi wako.